Mawu Amunsi
a Pa Yesaya 60:1, Baibulo la Dziko Latsopano linaseŵenzetsa mawu akuti “mkazi” m’malo moseŵenzetsa mawu akuti “Ziyoni” kapena “Yerusalemu.” Anasankha kucita zimenezi cifukwa mawu Aciheberi amene anawamasulila kuti “imilila” komanso akuti “onetsa kuwala” asonyeza kuti amakamba za munthu wamkazi amene akuchulidwa kuti “iwe.” Mawu akuti “mkazi” amathandiza amene akuŵelenga kuzindikila kuti mawu a mlembali akukamba za mkazi.