Mawu Amunsi
b M’bale J. F. Rutherford, amene anali kutsogolela Ophunzila Baibo pa nthawiyo, anali kudziŵika kuti “Judge” Rutherford. Zinali conco cifukwa asanayambe kutumikila pa Beteli, nthawi na nthawi anagwilapo nchito monga woweluza wapadela m’khoti la Eighth Judicial Circuit mu mzinda wa Missouri.