Mawu Amunsi
c Kuti Yehova ‘atithandize kukhalanso pa ubwenzi wabwino’ na iye, tiyenela kuonetsa kuti ndife olapa na kumupempha kuti atikhululukile macimo athu. Tiyenelanso kusintha makhalidwe athu. Tikacita chimo lalikulu, tiyenelanso kupempha thandizo kwa akulu mu mpingo.—Yak. 5:14, 15.