Mawu Amunsi a Ayuda anali kuchula Masalimo 113 mpaka 118 kuti Masalimo ya Haleluya. Ndipo anali kuimba nyimbozi potamanda Yehova.