Mawu Amunsi
a Yehova anali kukhululukila macimo a anthu amene analiko ngakhale Khristu asanapeleke dipo. Yehova anali kucita zimenezi cifukwa anali kumudalila Mwana wake kuti adzakhalabe wokhulupilika mpaka imfa. Telo kwa Yehova zinali ngati dipo linali litalipilidwa kale.—Aroma 3:25.