Mawu Amunsi
a Popeza Petulo sanali kubisa mmene anali kumvela, n’kutheka anafotokozela Maliko mmene Yesu anali kumvela komanso kucitila zinthu pa umoyo wake. Ici ciyenela kuti ndiye cifukwa cake Maliko anafotokoza kwambili mmene Yesu anali kumvela komanso kucitila zinthu.—Maliko 3:5; 7:34; 8:12.