Mawu Amunsi
a Patapita zaka ziwili ndi hafu Nikodemo atakambilana ndi Yesu, iye anali akali membala wa khoti yaikulu ya Ayuda. (Yoh. 7:45-52) Zolemba zina zakale zimati Nikodemo anakhala wophunzila Yesu atamwalila.—Yoh. 19:38-40.