Mawu Amunsi
c Hana popemphela anachula mau ofanana ndi amene Mose analemba. Mwacionekele, anali kupeza nthawi yosinkhasinkha Malemba. (Deut. 4:35; 8:18; 32:4, 39; 1 Sam. 2:2, 6, 7) Pambuyo pa zaka mahandiledi, Mariya, mai a Yesu, anakamba mau otamanda Mulungu ofanana kwambili ndi amene Hana anakamba.—Luka 1:46-55.