Mawu Amunsi
b Zioneka kuti Mariya Mmagadala anali mmodzi mwa azimai amene anali kuyenda ndi Yesu. Azimai amenewa anali kusamalila Yesu ndi atumwi ake pogwilitsa nchito cuma cao.—Mat. 27:55, 56; Luka 8:1-3.