Mawu Amunsi
a Yosefe anamwalila m’caka ca 1657 B.C.E. Mose anasankhidwa kukhala m’tsogoleli wa Aisiraeli ca m’ma 1514 B.C.E. Mwacionekele, pakati pa zaka ziwilizi m’pamene Yehova ndi Satana anali kukambilana za Yobu, ndipo m’pamenenso Yobu anakumana ndi mabvuto.