Mawu Amunsi
a Anthu amene anapulumuka, monga Baruki (mlembi wa Yeremiya), Ebedi-meleki Mwiitiyopiya, ndi Arekabu, sanali ndi cizindikilo ceniceni pamphumi pawo. (Yeremiya 35:1-19; 39:15-18; 45:1-5) Cizindikilo cimene anaikidwa cinali cophiphilitsa, ndipo cinali kutanthauza cabe kuti adzapulumuka.