LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO

Mawu Amunsi

b Zioneka kuti Akhristu amene analembako Baibo anali kuseŵenzetsa dzina la Mulungu akagwila mawu a “M’cipangano Cakale” okhala na dzinalo. Buku lina lakuti The Anchor Bible Dictionary linati: “Pali umboni woonetsa kuti poyamba, pamene Cipangano Catsopano cinali kulembedwa, zilembo zinayi zoimila dzina la Mulungu, Yahweh, zinali kupezeka pafupifupi m’malemba onse amene anagwila mawu cipangano cakale.” (Volume 6, tsamba 392) Kuti mudziŵe zambili onani nkhani yakuti “Dzina la Mulungu MʼMalemba a Chigiriki” pa Zakumapeto A5 mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika. M’Baibo yophunzilila yacingelezi pa Zakumapeto C2 pali mndandanda wa Mabaibo amene anaseŵenzetsa dzina la Mulungu pa Aroma 10:13.

Mabuku a m’Cinyanja (2000-2026)
Tulukani
Loŵani
  • Cinyanja
  • Gawilani
  • Makonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenela Kutsatila
  • Mfundo Yosunga Cisinsi
  • Kusunga Cinsinsi
  • JW.ORG
  • Loŵani
Gawilani