April Kabuku ka Msonkhano wa Umoyo ndi Utumiki Wathu Wacikristu, April 2016 Maulaliki Acitsanzo April 4-10 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 16-20 Limbikitsani Ena ndi Mau Abwino UMOYO WATHU WACIKRISTU Mbali Yatsopano Yoyambitsila Makambilano April 11-17 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 21-27 Yobu Anapewa Maganizo Olakwika April 18-24 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 28-32 Yobu Anali Citsanzo Cabwino Pankhani Yosunga Umphumphu April 25–May 1 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 33-37 Bwenzi Lenileni Limapeleka Uphungu Wolimbikitsa KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI Nchito Yogaŵila Tumapepala Toitanila Anthu ku Msonkhano Wacigawo UMOYO WATHU WACIKRISTU Zikumbutso za Msonkhano Wacigawo