August Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhiristu—Kabuku ka Misonkhano August 2016 Maulaliki a Citsanzo August 1-7 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 87–91 Khalanibe m’Malo Otetezeka a Wam’mwambamwamba CITANI KHAMA PA ULALIKI Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuthandiza Ophunzila Baibulo Kuti Adzipeleke ndi Kubatizika August 8-14 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 92-101 Amabala Zipatso Ngakhale ni Okalamba August 15-21 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 102-105 Yehova Amadziŵa Kuti Ndife Fumbi August 22-28 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 106-109 “Yamikani Yehova” August 29–September 4 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 110–118 “Yehova Ndidzamubwezela Ciani?” UMOYO WATHU WACIKHIRISTU Phunzitsani Coonadi UMOYO WATHU WACIKHIRISTU Kampeni Yapadela Yogaŵila Nsanja ya Mlonda mu September