December Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano December 2018 Makambilano Acitsanzo December 3-9 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 9-11 Wozunza Akhristu Mwankhaza Akhala Mlaliki Wokangalika December 10-16 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 12-14 Paulo na Baranaba Apanga Ophunzila Kumadela Akutali UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu Mu Ulaliki—Kuthandiza Anthu a “Maganizo Abwino” Kukhala Ophunzila December 17-23 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 15-16 Cigamulo Cozikidwa pa Mawu a Mulungu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Muziimba Mosangalala Nyimbo Zotamanda Yehova December 24-30 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 17-18 Tengelani Citsanzo ca Mtumwi Paulo Polalikila na Kuphunzitsa December 31–January 6 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 19-20 “Mukhale Chelu ndi Kuyang’anila Gulu Lonse la Nkhosa”