August Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano August 2019 Makambilano Acitsanzo August 5-11 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 TIMOTEYO 1-4 “Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Muziyanjana na Anthu Okonda Yehova August 12-18 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | TITO 1–FILIMONI “Kuika Akulu” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Acinyamata—Khalani “Odzipeleka pa Nchito Zabwino” August 19-25 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 1-3 Kondani Cilungamo, Danani Nako Kusamvela Malamulo August 26–September 1 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 4-6 Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Nchito Zabwino Zimene Sizidzaiŵalidwa