December Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano December 2020 Makambilano Acitsanzo December 7-13 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 10-11 Cikondi pa Yehova Ciyenela Kukhala Cacikulu Kuposa Cikondi pa Acibale UMOYO WATHU WACIKHRISTU Timaonetsa Cikondi Ngati Ticita Zinthu Mogwilizana na Cilango ca Yehova December 14-20 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 12-13 Phunzilamponi Kanthu pa Malamulo Okhudza Nthenda ya Khate December 21-27 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 14-15 Kulambila Koona Kumafuna Kukhala Oyela UMOYO WATHU WACIKHRISTU Pitilizani Kugaŵila Magazini December 28, 2020–January 3, 2021 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 16-17 Zimene Tingaphunzile pa Zocitika za pa Tsiku la Mwambo Wophimba Macimo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kodi Mungakonde Kufunsila Kuti Mukaloŵe Sukulu ya Alengezi a Ufumu?