July Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, July-August 2021 July 5-11 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambila Motani? CITANI KHAMA PA ULALIKI | WONJEZELANI CIMWEMWE CANU MU ULALIKI Onetsani Cifundo July 12-18 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka UMOYO WATHU WACIKHRISTU “Musamade Nkhawa” July 19-25 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mfundo Zothandiza Kuweluza Milandu Mwacilungamo July 26–August 1 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Moyo wa Munthu Ni Wamtengo Wapatali Kwa Yehova August 2-8 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Nyama CITANI KHAMA PA ULALIKI | WONJEZELANI CIMWEMWE CANU MU ULALIKI Afikeni Pamtima Anthu August 9-15 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amawadela Nkhawa Akazi UMOYO WATHU WACIKHRISTU Akazi Acikulile Muzicita Nawo Zinthu Monga Amayi Anu, Akazi Acitsikana Monga Azilongosi Anu August 16-22 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU ‘Madalitso Onsewa Adzakupeza’ UMOYO WATHU WACIKHRISTU Mmene Cilengedwe Cimaonetsela Cikondi ca Mulungu August 23-29 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kutumikila Yehova Sikovuta UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kukhala Wolimba Mtima Sikovuta August 30–September 5 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Tingaphunzile pa Mafanizo a m’Nyimbo Youzilidwa CITANI KHAMA PA ULALIKI Makambilano Acitsanzo