LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 123
  • Abusa Ndi Mphatso za Amuna

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Abusa Ndi Mphatso za Amuna
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Abusa ni Mphatso za Amuna
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Khulupilila Coonadi Iwe Mwini
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi
    Imbirani Yehova
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 123

Nyimbo 123

Abusa Ndi Mphatso za Amuna

(Aefeso 4:8)

1. Yehova amatithandiza

Kudzera mwa ’busa.

Mwa chitsanzo chawo chabwino

Amatsogolera.

(KOLASI)

Yehova watipatsa ’muna

Omwe tingadalire.

Amadera nkhawa za ife,

Ndiyetu tiwakonde.

2. Abusawa amatikonda,

Ndi okoma mtima.

Tikavulala amabwera

Kudzatichiritsa.

(KOLASI)

Yehova watipatsa ’muna

Omwe tingadalire.

Amadera nkhawa za ife,

Ndiyetu tiwakonde.

3. Safuna kuti tisochere,

Amatilangiza.

Kuti M’lungu tim’sangalatse

Pomutumikira.

(KOLASI)

Yehova watipatsa ’muna

Omwe tingadalire.

Amadera nkhawa za ife,

Ndiyetu tiwakonde.

(Onaninso Yes. 32:1, 2; Yer. 3:15; Yoh. 21:15-17; Mac. 20:28.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani