LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 January tsa. 5
  • Yehova Amakwanilitsa Malonjezo Ake

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Amakwanilitsa Malonjezo Ake
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 January tsa. 5

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZARA 1–5

Yehova Amakwanilitsa Malonjezo Ake

Yopulinta
Israelites rebuild the temple in Jerusalem

Yehova analonjeza kubwezeletsa kulambila koona pa kacisi ku Yerusalemu. Koma Aisiraeli atacoka ku ukapolo, anakumuna ndi zopinga zambili, kuonjezela pa lamulo la Mfumu loimitsa kumanga kacisi. Anthu ambili anali kuona monga sadzamaliza kumanga kacisi.

  1. c. 537 B.C.E.

    Koresi anapeleka lamulo lakuti kacisi afunika kumangidwanso

  2. 3:3

    Mwezi wa 7

    Guwa lansembe limangidwa; nsembe zipelekedwa

  3. 3:10, 11

    536 B.C.E.[2a]

    Maziko ayalidwa

  4. 4:23, 24

    522 B.C.E.[3a]

    Mfumu Aritasasita aimitsa nchito yomanga

  5. 5:1, 2

    520 B.C.E.[3b]

    Zekariya ndi Hagai analimbikitsa anthu kuyambilanso nchito yomanga

  6. 6:15

    515 B.C.E.[4]

    Kacisi amalizidwa

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani