LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsa. 8
  • Mtsikana Wacisulami n’Citsanzo Cabwino Cofunika Kutengela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mtsikana Wacisulami n’Citsanzo Cabwino Cofunika Kutengela
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi N’zotheka Kukhala m’Cikondi Ceniceni?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 November tsa. 8

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | NYIMBO YA SOLOMO 1-8

Mtsikana Wacisulami n’Citsanzo Cabwino Cofunika Kutengela

N’ciani cinam’pangitsa kukhala citsanzo cabwino kwa alambili a Yehova?

2:7; 4:12

Mtsikana wacisulami ali na atsikana a mu Yerusalemu
  • Anayembekezela mwamuna amene akanamukondadi

  • Anakana kuti ena amusonkhezele kukhala pa cisumbali na munthu aliyense amene anamufunsila

  • Anali wodzicepetsa, wofatsa, ndi wodziletsa

  • Sananyengeke na golide kapena mau okopa

Dzifunseni kuti:

‘Ni khalidwe liti la mtsikana wa cisulami limene niyenela kutengela?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani