LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 60
  • Ni Moyo Wawo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ni Moyo Wawo
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Ni Moyo Wawo
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso
    Imbirani Yehova
  • Mvela Udalitsike
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Khulupilila Coonadi Iwe Mwini
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 60

NYIMBO 60

Ni Moyo Wawo

Yopulinta

(Ezekieli 3:17-19)

  1. 1. Ino ni nthawi

    yocenjeza dziko lonse,

    Kuti tsiku la M’lungu wathu

    likubwela.

    (KOLASI)

    Akamvela, na kulapa;

    Adzapulumutsidwa.

    Nafe tidzapulumuka,

    Tikalalikila mau,

    Kwa onse.

  2. 2. Tili na uthenga,

    wouza anthu onse.

    Tiitane anthu

    abwelele kwa M’lungu.

    (KOLASI)

    Akamvela, na kulapa;

    Adzapulumutsidwa.

    Nafe tidzapulumuka,

    Tikalalikila mau,

    Kwa onse.

    (BILIJI)

    Kwa onse tilengeze,

    Tisacedwe, tiŵauze.

    Amvele, aphunzile;

    Kuti akapeze moyo.

    (KOLASI)

    Akamvela, na kulapa;

    Adzapulumutsidwa.

    Nafe tidzapulumuka,

    Tikalalikila mau,

    Kwa onse.

(Onaninso 2 Mbiri 36:15; Yes. 61:2; Ezek. 33:6; 2 Ates. 1:8.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani