NYIMBO 93
Dalitsani Misonkhano Yathu
Yopulinta
(Aheberi 10:24, 25)
1. Tidalitseni Yehova
Pamene tisonkhana.
Timakonda misonkhano;
Mzimu ukhale nafe.
2. Tipatseni Mau anu
Kuti atiyeletse.
Tilalikile kwa onse;
Tikhale na Cikondi.
3. Tidalitseni Yehova;
Tikhale na mtendele.
Mau na zocita zathu
Zikulemekezeni.
(Onaninso Sal. 22:22; 34:3; Yes. 50:4.)