Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2017
Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo
BAIBO
- Umboni Winanso (Tatenai analikodi), Na. 3 
- Elias Hutter na ma Baibo Ake a Ciheberi, Na. 4 
- Pindulani na Zimene Mumaŵelenga m’Baibo, Na. 1 
- Kuphonya pa Kamvedwe, Na. 1 
- N’cifukwa Ciani Pali Osiyana-siyana? Na. 6 
BAIBO IMASINTHA ANTHU
- N’nali Kukhulupilila Kuti Kulibe Mulungu (A. Golec), Na. 5 
- N’nali Kuopa Imfa (Y. Quarrie), Na. 1 
- N’nali Kukonda Baseball Kuposa Cina Ciliconse (S. Hamilton), Na. 3 
UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU
- Kupatsa Kumapindulitsa, Na. 2 
- Kuti Munthu Akhale Mtumiki, Kodi Afunika Kukhala Wosakwatila? Na. 2 
- Kodi Akhristu Ayenela Kukondwelela Khrisimasi? Na. 6 
- Cikondi—Khalidwe Lamtengo Wapatali, Aug. 
- Kuona Zolakwa Moyenelela, Na. 6 
- Kuthetsa Mkangano ndi Kulimbikitsa Mtendele, June 
- Pakacitika Zinthu Zimene Zingasokoneze Ubwenzi, Mar. 
- Kupambana Nkhondo Yoteteza Maganizo Anu, July 
YEHOVA
MBONI ZA YEHOVA
- Kujaila mu Mpingo Wanu Watsopano, Nov. 
- “Wopatsa Mowolowa Manja Adzadalitsidwa” (zopeleka), Nov. 
- Umoyo Wosalila Zambili Umabweletsa Cimwemwe, May 
- “Khote-khote Ngwanjila, Palinga Mtima Mpomwepo” (Australia), Feb. 
- Anadzipeleka ku Turkey, July 
- Anadzipeleka na Mtima Wonse (alongo osakwatiwa), Jan. 
- Kuonetsa Kukoma Mtima Kamodzi Cabe, Oct. 
- “N’liti Pamene Tidzakhala na Msonkhano Wina Waukulu?” (Mexico), Aug. 
- ‘Cangu na Cikondi Zinawonjezeka Kwambili’ (msonkhano wacigawo mu 1922), May 
YESU KHRISTU
- Kodi Yesu Ananyoza Pokamba Fanizo la “Tiagalu”? Na. 5 
- Kodi Yesu Anali Kuoneka Bwanji Kweni-kweni? Na. 6 
MBILI YANGA
- Kukhala Wogontha Sikunanilepheletse Kuphunzitsa Ena (W. Markin), May 
- Kucita Zimene Yehova Watilamula Kumabweletsa Madalitso (O. Matthews), Oct. 
- N’natsimikiza Mtima Kukhala Msilikali wa Khristu (D. Psarras), Apr. 
- Kupilila Ziyeso Kumabweletsa Madalitso (P. Sivulsky), Aug. 
- Nakhala na Mwayi Wotumikila Pamodzi ndi Amuna Auzimu (D. Sinclair), Sept. 
- Napindula Cifukwa Coyenda ndi Anthu Anzelu (W. Samuelson), Mar. 
- N’nasiya Zinthu Zina Pofuna Kutsatila Ambuye (F. Fajardo), Dec. 
- Tinaona Cisomo ca Mulungu m’Njila Zambili (D. Guest), Feb. 
NKHANI ZOSIYANA-SIYANA
- Kodi Angelo Aliko Zoona? Na. 5 
- Nkhawa, Na. 4 
- Mphatso Yoposa Zonse, Na. 6 
- Dzina la m’Baibo pa Mtsuko Wakale, Mar. 
- “Udalitsike Cifukwa ca Kulingalila Bwino Kwako” (Abigayeli), June 
- Kumasuka mu Ukapolo, Na. 2 
- Zidzatheka Kuti Padzikoli Pakhale Mtendele? Na. 5 
- Kodi zidzatheka kuti padziko lapansi pakhale cilungamo ceni-ceni? Na. 3 
- Amuna Anayi Okwela pa Mahosi, Na. 3 
- Mulungu Anamucha Mfumukazi (Sara), Na. 5 
- Kacilembo Kocepetsetsa Kaciheberi, Na. 4 
- ‘Mulungu Anakondwela Naye’ (Inoki), Na. 1 
- Mmene Gayo Anathandizila Abale Ake, May 
- Kodi Moto Unali “Kunyamuliwa” Bwanji M’nthawi Zakale? Jan. 
- Yosefe wa ku Arimateya, Oct. 
- Kodi Tili mu “Masiku Otsiliza”? Na. 2 
- Musamaone Cabe Maonekedwe, June 
- Paradaiso Padziko Lapansi—Ni Yeni-yeni Kapena ni Maloto Cabe? Na. 4 
- Malangizo a Paulo Akuti Asapitilize Ulendo wa Pamadzi (Mac. 27), Na. 5 
- Mavuto, Na. 1 
- Kodi Amalonda Amene Anali Kugulitsa Ziweto M’kacisi Anali “Acifwamba”? June 
- “Ndiwe Mkazi Wokongola m’Maonekedwe Ako” (Sara), Na. 3 
- Kodi Aramagedo n’ciani? Na. 6 
- Kodi Ayuda Anali na Cizoloŵezi Canji Cimene Cinapangitsa Yesu Kuwaletsa Kulumbila? Oct. 
- Kodi Baibo Imati Ciani pa Nkhani ya Moyo na Imfa? Na. 4 
- Munthu Amene Mukonda Akadwala Matenda Osacilitsika, Na. 4 
MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA
- Yehova “sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapilile” (1 Akor. 10:13), Feb. 
- Kodi n’koyenela Mkhristu kukhala na mfuti yodzitetezela kwa anthu ena? July 
- Kodi Kukhala pa Mzela wa Makolo a Mesiya Kunadalila Kukhala Oyamba Kubadwa? Dec. 
- Kodi Akhristu apabanja ayenela kuona kuti kuseŵenzetsa ma IUD ni njila ya cilezi yogwilizana na Malemba? Dec. 
- N’cifukwa ciani zimene Mateyu na Luka analemba zokhudza umoyo wa Yesu ali mwana zimasiyana? Aug. 
NKHANI ZOPHUNZILA
- Kodi Mumathaŵila kwa Yehova? Nov. 
- Kodi Mudzayembekezela Moleza Mtima? Aug. 
- ‘Limba Mtima, Ugwile Nchito Mwamphamvu,’ Sept. 
- Magaleta na Cisoti Cacifumu Zimakutetezani, Oct. 
- Phunzilani Kukhala Wodziletsa, Sept. 
- Musalole Kuti Cikondi Canu Cizilale, May 
- “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?” May 
- Kodi Mumacita Zinthu Mogwilizana ndi Cilungamo ca Yehova? Apr. 
- Khalani ndi Cikhulupililo Ndipo Muzipanga Zosankha Mwanzelu, Mar. 
- Muzilemekeza Amene Afunika Kulandila Ulemu, Mar. 
- Kuthandiza Alendo Ocokela ku Mayiko Ena “Kutumikila Yehova Mokondwela,” May 
- Kuthandiza Ana a Alendo Ocokela m’Dziko Lina, May 
- Mmene Timavalila Umunthu Watsopano ndi Kusauvulanso, Aug. 
- Mmene Timavulila Umunthu Wakale ndi Kusauvalanso, Aug. 
- “Ine Ndili Ndi Ciyembekezo mwa Mulungu,” Dec. 
- “Ndidziŵa Kuti Adzauka,” Dec. 
- Tengelani Khalidwe la Yehova la Cifundo, Sept. 
- Tengelani Cilungamo ca Yehova na Cifundo Cake, Nov. 
- Yehova Amatsogolela Anthu Ake, Feb. 
- Yehova Amatitonthoza m’Masautso Athu Onse, June 
- Colinga ca Yehova Cidzakwanilitsika, Feb. 
- Muziika Maganizo Anu pa Nkhani Yaikulu, June 
- Musalole Ciliconse Kukumanitsani Mphoto, Nov. 
- “Tizisonyezana Cikondi Ceni-ceni m’Zocita Zathu,” Oct. 
- Muziimba Mosangalala! Nov. 
- Mulungu “Akwanilitse Zofuna Zanu,” July 
- Yehova Atamandike Cifukwa ca Kudzipeleka Kwanu! Apr. 
- Makolo—Thandizani Ana Anu Kupeza ‘Nzelu Zowathandiza Kuti Adzapulumuke,’ Dec. 
- N’cifukwa Ciani Tifunika Kutamanda Yehova? July 
- Pewani Kutengela Maganizo a Dziko, Nov. 
- Kufunafuna Cuma Ceni-ceni, July 
- Tumikilani Yehova ndi Mtima Wathunthu, Mar. 
- Ikani Mtima Wanu pa Cuma Cauzimu, June 
- “Woweluza wa Dziko Lonse” Amacita Cilungamo Nthawi Zonse, Apr. 
- “Mtendele wa Mulungu . . . Umaposa Kuganiza Mozama Kulikonse,” Aug. 
- Dipo—‘Mphatso Yangwilo’ Yocokela kwa Atate, Feb. 
- ‘Zimenezo Uziphunzitse kwa Amuna Okhulupilika,’ Jan. 
- Coonadi ‘Sicibweletsa Mtendele Koma Lupanga,’ Oct. 
- “Mau a Mulungu . . . Ndi Amphamvu,” Sept. 
- “Mau a Mulungu Wathu Adzakhala Mpaka Kalekale,” Sept. 
- Muziyamikila Mphatso Yanu ya Ufulu Wosankha Zocita, Jan. 
- “Khulupilila Yehova Ndipo Cita Zabwino,” Jan. 
- Muzicilikiza Ulamulilo wa Yehova, June 
- Mmene Masomphenya a Zekariya Amakukhudzilani, Oct. 
- “Lilani Ndi Anthu Amene Akulila”, July 
- Kodi Cidzacokapo N’ciani Ufumu wa Mulungu Ukadzabwela? Apr. 
- ‘Muzikwanilitsa Zimene Mwalonjeza,’ Apr. 
- N’ndani Akutsogolela Anthu a Mulungu Masiku Ano? Feb. 
- N’cifukwa Ciani Kudzicepetsa N’kofunikabe? Jan. 
- Kodi Mudzatengelapo Phunzilo pa Zimene Zinalembedwa? Mar. 
- Mukhoza Kukhalabe Wodzicepetsa Ngakhale pa Ciyeso, Jan. 
- Acicepele—“Pitilizani Kukonza Cipulumutso Canu,” Dec.