Onani Nkhanizi Pa Jw.Org
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
N’chifukwa Chiyani Ndimangolankhula Zolakwika?
Kodi n’ciyani cingakuthandizeni kuti mumbakumbuke mukanati kulewa cinthu?
Pitani pa jw.org, pomwe padanemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZISA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Kodi Ndingatani Ngati Nditamva Kuti Mwana Wanga Amavutitsidwa ndi Anzake?
Nfundo zinai zomwe zingakuthandizeni kupfunzisa mwana wanu momwe angatawirire anzace akamuzunza.
Pitani pa jw.org, pomwe padanemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZISA > ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA > KULERA ANA.