Onani Nkhanizi Pa Jw.Org
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Luso la Gulugufe Woyera Lotha Kuimitsa Mapiko Ake Ngati V
Kodi bemphenwa m’cena akuthandiza tani masiyentista kuti akonze mitcini yakugasira maluju yomwe imbaphata basa na dzuwa?
Pitani pa jw.org, pomwe padanemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZISA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Zimene Mungachite Ngati Mumaona Zinthu Mosiyana
Kodi anyakulowolana angamalise tani mabvuto acipitiriza kukhala pa mtendere?
Pitani pa jw.org, pomwe padanemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZISA > ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA > ANTHU OKWATIRANA.