Mafala ya m'nyantsi
c Kuti mudziwe nfundo zinango zakulewa momwe mungamalisire bvuto lakusenzekesa cidzo, onani nkhani yakuti “Zimene Achinyamata Amadzifunsa . . . Kodi Ndingathetse Bwanji Chizolowezi Chimenechi?” mu Galamukani! ya Novembro, 2006 na m’bukhu lakuti Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Volume 1, pa tsamba 178 mpaka 182.