Mafala ya m'nyantsi
b Mungagumane nkhani zomwe zingathandize mabanja pa jw.org pa mbali yakuti “Mfundo zothandiza mabanja.” Nkhani zinango zomwe ziripo pa mbaliyi kwa anyakulowolana ni izi: “Kodi Mungasonyezane Bwanji Ulemu?” na “Kodi Mungasonyeze Bwanji kuti Mumayamikira Zimene Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Amachita?”; kwa abereki: “Phunzitsani Ana Anu Kugwiritsa Ntchito Foni Mosamala” na “Zimene Mungachite Kuti Muzimasukirana ndi Mwana Wanu”; ndipo kwa maswaka: “Kodi Mungatani Kuti Musamangotengera Zochita za Anzanu?” na “Kodi Mungatani Ngati Mumasowa Wocheza Naye?”