LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • es24 tsa. 6
  • Moseŵenzetsela Kabuku Kano

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Moseŵenzetsela Kabuku Kano
  • Kusanthula Malemba Tsiku na Tsiku—2024
  • Tumitu
Kusanthula Malemba Tsiku na Tsiku—2024
es24 tsa. 6

Moseŵenzetsela Kabuku Kano

Pa mapeji otsatila, mudzapezapo lemba la tsiku lililonse na ndemanga yake. Ngakhale kuti mungaŵelenge lemba na ndemanga yake nthawi iliyonse, ambili amakonda kuŵelenga m’maŵa, cifukwa kumawathandiza kumaganizilapo pa lembalo tsiku lonse. Kukambilana lemba monga banja n’kopindulitsa ngako. Mabanja a Beteli zungulile dziko lapansi amacita zimenezi pa cakudya cam’maŵa.

Ndemanga zake zinatengedwa mu Nsanja ya Mlonda (w) ya April 2022 mpaka March 2023. Nambala yotsatila deti ya Nsanja ya Mlonda ni nambala ya peji (mapeji) m’magazini imeneyo, ndiyeno pabwela manambala a ndime mmene mwacokela ndemangayo (Onani citsanzo pansipa.) Mungaŵelenge mfundo zina zowonjezela m’nkhani yonse.

[Cithunzi pa tsamba 6]

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani