‘Mverani Zimene Mzimu Ukunena ku Mipingo.’
CHIVUMBULUTSO 3:22
M’mawa
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero
9:00 Tingaonetse Motani Kuti ‘Timamvera Zimene Mzimu Ukunena ku Mipingo?’
9:15 “Iwe . . . Sunafooke”
9:30 “Usacite Mantha”
9:55 Nyimbo Na. 73 ndi Zilengezo
10:05 “Sunakane Kuti Umandikhulupirira”
10:35 Ubatizo: Cifukwa Cake Ubatizo Wanu ndi Wofunika
11:05 Nyimbo Na. 79
Masana
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 126
12:35 Zocitika
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Nkhani Yosiyirana: Mmene Tingagwilitsire Nchito Uphungu
• “Gwirani Mwamphamvu Zinthu Zabwino Zimene Muli Nazo”
• ‘Khalani Maso, Ndipo Limbikitsani Otsala’
• “Ndatsegula Khomo Pamaso Pako”
14:00 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo
14:10 Khalani “Odzipereka”
14:55 Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero