Loŵani mu Mpumulo wa Mulungu!
AHEBERI 4:11
M’maŵa
08:40 Nyimbo Zamalimba
08:50 Nyimbo Na. 87 na Pemphelo
09:00 Loŵani mu Mpumulo wa Mulungu —Motani?
09:15 Kodi “Mawu a Mulungu ndi Amoyo”—M’njila Yotani?
09:30 Pitilizani Kudalila Yehova Kuti Akutsogoleleni
09:55 Nyimbo Na. 89 na Zilengezo
10:05 Yehova Amadalitsa anthu Omvela
10:35 Kudzipatulila na Ubatizo
11:05 Nyimbo Na. 32
Masana
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 49
12:35 Zocitika
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Nkhani Yosiyilana: Amakondweletsa Mtima wa Yehova!
• Acinyamata
• Alongo
• Okalamba
14:00 Nyimbo Na. 38 na Zilengezo
14:10 Pezani Cimwemwe mu Utumiki Wanu kwa Yehova
14:55 Nyimbo Na. 118 na Pemphelo