Kondweletsani Mtima wa Yehova
Miyambo 27:11
KUM’MAŴA
8:30 Nyimbo Zamalimba
8:40 Nyimbo Na. 29 na Pemphelo
8:50 Kondweletsani Mtima wa Yehova
9:05 Yosiilana: Kutengela Makhalidwe Anayi a Yehova
• Cilungamo
• Moseŵenzetsela Mphamvu
• Nzelu
• Cikondi
10:05 Nyimbo Na. 81 na Zilengezo
10:15 Lemekezani Mulungu mwa “Kubala Zipatso Zambili”
10:30 Kudzipatulila na Ubatizo
11:00 Nyimbo Na. 49
KUMASANA
12:10 Nyimbo Zamalimba
12:20 Nyimbo Na. 28 na Pemphelo
12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Mungamukondweletse Mulungu—Motani?
13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:30 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo
13:40 Yosiilana: Muzikondweletsa Yehova . . .
• Pa Umoyo Wanu
• M’banja Mwanu
• Mumpingo Mwanu
• M’dela Lanu
14:40 “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Mphamvu Yanu”
15:15 Nyimbo Na. 110 na Pemphelo