Banja la Yehova Logwilizana
AEFESO 4:3
M’maŵa
08:30 Nyimbo Zamalimba
08:40 Nyimbo Na. 85 na Pemphelo
08:50 Muziyamikila Malo Anu m’Banja la Yehova
09:05 Yosiyilana: Anapangitsa Ena Kumva Kuti ni Olandilidwa
• Elihu
• Lidiya
• Yesu
10:05 Nyimbo Na. 100 na Zilengezo
10:15 Pitilizani Kuthandiza Ena Kuti Akhale m’Banja la Yehova
10:30 Kudzipatulila Komanso Ubatizo
11:00 Nyimbo Na. 135
Masana
12:10 Nyimbo Zamalimba
12:20 Nyimbo Na. 132 na Pemphelo
12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Kodi Banja Lanu ni Malo a Mpumulo Komanso a Mtendele?
13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:30 Nyimbo Na. 136 na Zilengezo
13:40 Yosiyilana: Kodi Mungakhale Bwanji Wolimbikitsa Mtendele?
• Lankhulani Mawu “Olimbikitsa”
• ‘Yendani m’Cikondi’
• Kanizani Adani Athu
14:40 ‘Musaleke Kuyamika Mulungu Cifukwa ca’ Banja Lanu Lauzimu
15:15 Nyimbo Na. 107 na Pemphelo