“Cikondi Cimamangilila”
KUM’MAŴA
8:30 Nyimbo Zamalimba
8:40 Nyimbo Na. 90 na Pemphelo
8:50 “Kudziŵa Zinthu Kumacititsa Munthu Kudzitukumula, Koma Cikondi Cimamangilila”
9:05 Yosiilana: Analimbikitsa Ena
Baranaba
Paulo
Dorika
10:05 Nyimbo Na. 79 na Zilengezo
10:15 Muzionetsa Cikondi Polalikila Uthenga Wabwino
10:30 Kudzipatulila na Ubatizo
11:00 Nyimbo Na. 52
KUMASANA
12:10 Nyimbo Zamalimba
12:20 Nyimbo Na. 107 na Pemphelo
12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Kodi Cikondi Ceni-ceni Cimacilikiza Bwanji Coonadi?
13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:30 Nyimbo Na. 101 na Zilengezo
13:40 Yosiilana: Thandizani Kuti Thupi Lonse Likule
Muzikonda Coonadi ca m’Baibo
Muzicilikiza Malamulo Anzelu a Mulungu
Muzilimbikitsa Akhristu Anzanu
14:40 “Zonse Zimene Mukucita, Muzicite Mwacikondi”
15:15 Nyimbo Na. 105 na Pemphelo