Onetsani Cikhulupililo!
M’MAŴA
8:30 Nyimbo Zamalimba
8:40 Nyimbo Na. 118 na Pemphelo
8:50 Onetsani Cikhulupililo!—Motani, Cifukwa Ciani?
9:05 Yosiyilana: Tengelani Citsanzo ca Amene Anaonetsa Cikhulupililo
• Isaki na Rabeka
• Esitere
• Timoteyo
10:05 Nyimbo Na. 60 na Zilengezo
10:15 “Tili ndi Cikhulupililo, Cotelo Tikulankhula”
10:30 Kudzipatulila na Ubatizo
11:00 Nyimbo Na. 52
MASANA
12:10 Nyimbo Zamalimba
12:20 Nyimbo Na. 9 na Pemphelo
12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Onetsani Cikhulupililo mwa Mulungu “Amene Sanganame”
13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:30 Nyimbo Na. 54 na Zilengezo
13:40 Yosiyilana: ‘Yendani mwa Cikhulupililo’ Tsiku Lililonse
• “Musamade Nkhawa”
• “Muzigwilitsa Nchito Bwino Nthawi Yanu”
• Pitilizani Kusakhala “Mbali ya Dziko”
14:40 “Yehova Amadziŵa Anthu Ake”
15:15 Nyimbo Na. 7 na Pemphelo