Mlozela Nkhani Nsanja ya Mlonda ya 2013
Woonetsa deti ya magazini mmene nkhaniyo ili
BAIBO
Kodi Baibo Limanena Ciani? 10/1
MBONI ZA YEHOVA
M’bale Watsopano wa m’Bungwe Lolamulila (M. Sanderson) 7/1
MOYO NDI MIKHALIDWE YACIKRISTU
Banja Lingakhale Lacimwemwe ndi Lolimba, 9/1
Pambuyo Polekana, 10/1
NKHANI ZOPHUNZILA
Abusa Tsanzilani M’busa Wamkulu, 11/1
Cilengedwe Cimadziŵikitsa Mulungu Wamoyo, 10/1
‘Citani Zimenezi Pondikumbukila,’ 12/1
Citani Zinthu Mogwilizana ndi Pemphelo la Yesu, 10/1
“Dziŵani Kuti Ine Ndili Pamodzi Ndi Inu Masiku Onse, 7/1
Ganizilanani ndi Kulimbikitsana, 8/1
Ganizilani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenela Kukhala, 8/1
‘Ici Cidzakhala Cikumbutso kwa Inu,’ 12/1
“Khalani Maso Kuti Musanyalanyaze Kupemphela,” 11/1
Kodi Abusa 7 ndi Atsogoleli 8 Ndani Masiku Ano? 11/1
Kodi Mudzapeleka Nsembe Kaamba ka Ufumu? 12/1
Kodi Mwasandulika? 9/1
Kondwelani Ndi Zikumbutso za Yehova, 9/1
Kudyetsa Anthu Ambili mwa Kugwilitsila Nchito Anthu Ocepa, 7/1
Mmene Tingayembekezele Mulungu Moleza Mtima, 11/1
“Musafulumile Kugwedezeka pa Maganizo Anu” 12/01
‘Musakwiile Yehova,’ 8/1
Muzimvela Abusa a Yehova, 11/1
Mwapatulidwa, 8/15
“Ndani Kweni-kweni Amene Ali Kapolo Wokhulupilika ndi Wanzelu?,” 7/1
Pangani Zosankha Zanu Mwanzelu, 9/1
“Tiuzeni, Kodi Zinthu Zimenezi Zidzacitika Liti? 7/1
Tumikilani Yehova Monga Akapolo, 10/1
Upainiya Umalimbitsa Unansi Wathu ndi Mulungu, 9/1
Zikumbutso za Yehova Ndi Zodalilika, 9/1
NKHANI ZOSIYANA-SIYANA
Moyo Wamuyaya, 7/1
Anam’sunga “Pom’pulumutsa Pamodzi ndi Anthu Ena” (Nowa), 8/1
Kodi Zamalisece Zilibe Vuto? 8/1
Ciukililo, 10/1
Kodi Muyenela Kukhulupilila Cipembedzo? 7/1
N’cifukwa Ciani Kupita Kumwamba? 11/1
N’cifukwa Ciani Pali Mavuto Ambili? 9/1
YEHOVA
Kodi Mulungu Ndi Wofunika kwa Ife? 12/1
Mabodza Amene Amalepheletsa Anthu Kukonda Mulungu, 11/1
Kodi Mulungu Amamva Mapemphelo Onse? 8/1
‘Zinthu Zonse Zimene ndi Kupanga N’zatsopano,’ 12/1
YESU KRISTU
Kodi Tiyenela Kumukumbukila Bwanji?
Kubwelanso kwa Yesu, 12/1