Zamkati
March 1, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI ZOPHUNZILA
MAY 5-11, 2014
TSAMBA 7 • NYIMBO: 61, 25
MAY 12-18, 2014
Mmene Tingakhalilebe ndi Maganizo Oyenela
TSAMBA 12 • NYIMBO: 74, 119
MAY 19-25, 2014
Muzilemekeza Okalamba Amene Ali Pakati Panu
TSAMBA 17 • NYIMBO: 90, 135
MAY 26, 2014–JUNE 1, 2014
TSAMBA 22 • NYIMBO: 134, 29
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Mmene Tingakhalilebe ndi Maganizo Oyenela
Tili ndi mdani amene mwamacenjela angaononge mzimu wathu wodzimana. Nkhani ino ifotokoza mdani ameneyu ndipo ionetsa mmene tingagwilitsilile nchito Baibulo kumugonjetsa.
▪ Mmene Tingakhalilebe ndi Maganizo Oyenela
Maganizo oyenela amatithandiza kupitilizabe kulambila Yehova. Nanga n’cifukwa ciani ena amavutika ndi maganizo olakwika? Nkhani ino ionetsa mmene Baibulo lingatithandizile kuti tizidzionabe moyenela.
▪ Muzilemekeza Okalamba Amene Ali Pakati Panu
▪ Muzisamalila Okalamba
Nkhani zimenezi zidzaonetsa udindo wa Mkristu aliyense ndiponso wa mpingo wosamalila Akristu anzathu ndi acibale okalamba. Tidzaonanso mfundo zothandiza zimene zingatithandize kukwanilitsa udindo umenewu.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
26 Cocitika Cimene Simuyenela Kuphonya
27 Kulambila kwa Pabanja—Zimene Mungacite Kuti Kukhale Kosangalatsa Kwambili