Zamkati
June 1, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI ZOPHUNZILA
AUGUST 4-10, 2014
“Uzikonda Yehova Mulungu Wako”
TSAMBA 7 • NYIMBO: 3, 65
AUGUST 11-17, 2014
“Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondela Wekha”
TSAMBA 12 • NYIMBO: 84, 72
AUGUST 18-24, 2014
Kodi Mumaona Zofooka za Anthu Mmene Yehova Amazionela?
TSAMBA 17 • NYIMBO: 77, 79
AUGUST 25-31, 2014
Thandizani Ena Kupita Patsogolo
TSAMBA 22 • NYIMBO: 42, 124
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ “Uzikonda Yehova Mulungu Wako”
▪ “Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondela Wekha”
Nkhani ziŵili izi zifotokoza malamulo aakulu aŵili a m’Cilamulo amene Yesu anachula. Tidzaphunzila zimene Yesu anatanthauza pamene anakamba kuti tiyenela kukonda Yehova ndi mtima wathu wonse, moyo wathu wonse, ndi maganizo athu onse. Onani zimene tingacite kuti tionetse kuti timakonda anzathu mmene timadzikondela.
▪ Kodi Mumaona Zofooka za Anthu Mmene Yehova Amazionela?
▪ Thandizani Ena Kupita Patsogolo
Tingawathandize motani anthu amene amadziona kuti ndi ofooka? Iyi ndi mbali ina imene tidzakambitsilana m’nkhani zimenezi. Ndiponso, nkhanizi zidzaonetsa mmene tingathandizile abale acinyamata kapena obatizika catsopano kupita patsogolo..
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
Kodi Mulungu Amakuona Bwanji Kukoka Fodya? 4
Kodi Munadyapo Mkate wa Moyo? 27