Zamkati
February 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
YOPHUNZILA
APRIL 6-12, 2015
Khalani Wodzicepetsa ndi Wacifundo Monga Yesu
TSAMBA 5 • NYIMBO: 5, 84
APRIL 13-19, 2015
Khalani Wolimba Mtima ndi Wozindikila Monga Yesu
TSAMBA 10 • NYIMBO: 99, 108
APRIL 20-26, 2015
Kukonzekeletsa Anthu ‘Kuphunzila Zokhudza Yehova’
TSAMBA 19 • NYIMBO: 98, 104
APRIL 27, 2015–MAY 3, 2015
Yehova Akutsogolela Nchito Yathu Yophunzitsa Padziko Lonse
TSAMBA 24 • NYIMBO: 103, 66
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Khalani Wodzicepetsa ndi Wacifundo Monga Yesu
▪ Khalani Wolimba Mtima ndi Wozindikila Monga Yesu
Baibulo limatilimbikitsa kutsatila mapazi a Yesu mosamala kwambili. (1 Pet. 2: 21) Popeza ndife opanda ungwilo, kodi n’zotheka kutsatila citsanzo cangwilo ca Yesu? Nkhani yoyamba pa nkhani ziŵili izi idzafotokoza mmene tingakhalile odzicepetsa ndi acifundo monga Yesu. Nkhani yaciŵili idzaonetsa mmene tingatengele citsanzo cake pankhani yokhala wolimba mtima ndi wozindikila.
▪ Kukonzekeletsa Anthu ‘Kuphunzila Zokhudza Yehova’
▪ Yehova Akutsogolela Nchito Yathu Yophunzitsa Padziko Lonse
Nkhani yoyamba pa nkhani ziŵili izi idzafotokoza mmene Yehova anathandizila ophunzila a Yesu m’nthawi ya atumwi kulalikila uthenga wabwino. M’nkhani yotsatila, tidzakambilana zinthu zina zamakono zimene zatithandiza kufalitsa uthenga wa Ufumu kwa anthu a mitima yabwino padziko lonse lapansi.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
3 Mphatso Yosangalatsa ya Anthu a ku Japan
15 Pitilizani Kukhala Wacangu mu Utumiki
PA CIKUTO: Akugaŵila magazini a Galamukani! mu ulaliki wa kunyumba ndi nyumba pacilumba ca Bali, ndipo alandilidwa mogwilizana ndi cikhalidwe ca ku Indonesia
KU INDONESIA
KULI ANTHU
237,600,000
OFALITSA
24,521
APAINIYA A NTHAWI ZONSE
2,472
Kuli apainiya apadela 369 amene akutumikila pa zilumba zosiyanasiya zokwana 28