LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w15 5/1 tsa. 12
  • Kukumbukila Imfa ya Yesu—Liti Ndipo Kuti?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kukumbukila Imfa ya Yesu—Liti Ndipo Kuti?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Nkhani Zofanana
  • Cocitika Cimene Simuyenela Kuphonya
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Yehova Amadalitsa Kuyesetsa Kwathu Kuti Ticite Cikumbutso
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Kuyankha Mafunso A m’Baibulo
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Mudzacitapo Ciani pa Mphatso ya Mulungu Yopambana Zonse?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
w15 5/1 tsa. 12

Kukumbukila Imfa ya Yesu—Liti Ndipo Kuti?

Pa usiku wakuti aphedwa maŵa, Yesu analamula ophunzila ake kukumbukila nsembe imene anali pafupi kupeleka. Iye anati: “Muzicita zimenezi pondikumbukila.”—Luka 22:19.

Caka cino, Cikumbutso ca imfa ya Yesu cidzakhalako pa Cisanu, April 3 dzuŵa litaloŵa. Mboni za Yehova zikukuitanani pamodzi ndi banja lanu kuti mudzamvetsele nkhani imene idzafotokoza cifukwa cake imfa ya Yesu ndi yofunika kwambili ndiponso mmene mungapindulile ndi imfa yake.

Kuti mudziŵe nthawi ndi malo amene kudzacitikila mwambo wosalipilitsa umenewu, mungafunse wa Mboni za Yehova kwanuko kapena mungapite pa webusaiti yathu ya www.jw.org.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani