Zamkati
March 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
YOPHUNZILA
MAY 4-10, 2015
“Munavomeleza Kuti Zimenezi Zicitike”
TSAMBA 7 • NYIMBO: 65, 64
MAY 11-17, 2015
TSAMBA 12 • NYIMBO: 108, 24
MAY 18-24, 2015
Zimene Tiphunzilapo pa Fanizo la Matalente
TSAMBA 19 • NYIMBO: 101, 116
MAY 25-31, 2015
Kuthandiza Abale a Kristu Mokhulupilika
TSAMBA 25 • NYIMBO: 107, 63
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ “Munavomeleza Kuti Zimenezi Zicitike”
▪ Kodi ‘Mudzakhalabe Maso’?
M’nkhani yoyamba, tidzakambilana mmene Yehova wakhala akutsogolela anthu ake kuphunzila zinthu pang’onopang’ono m’njila yosavuta ndi yomveka bwino. M’nkhani yaciŵili, tidzakambilana fanizo la Yesu la anamwali 10 ndi kuona mmene lingatithandizile kukhala maso mwakuuzimu masiku ano.
▪ Zimene Tiphunzilapo pa Fanizo la Matalente
▪ Kuthandiza Abale a Kristu Mokhulupilika
Pofotokoza cizindikilo ca kukhalapo kwake, Yesu anakamba mafanizo aŵili amene tidzakambilana. Fanizo loyamba ndi lokhudza akapolo amene anapatsidwa matalente, ndipo lina ndi lokhudza mmene anthu adzalekanitsidwila monga nkhosa ndi mbuzi. Tidzaphunzila cifukwa cake Yesu anafotokoza mafanizo amenewa ndi mmene amatikhudzila.
PACIKUTO: Anthu ambili amapita ku Copán kukaona mabwinja ocititsa cidwi, koma Mboni za Yehova kumeneko zimathandiza anthu kuyembekezela zinthu zabwino mtsogolo
KU HONDURAS
KULI ANTHU
8,111,000
OFALITSA
22,098
APAINIYA ANTHAWI ZONSE
3,471
Cinenelo cacikulu ku Honduras ndi Cisipanishi. Koma ofalitsa 365 m’mipingo 12 amagwilitsila nchito cinenelo cochedwa Garifuna. Kulinso mipingo 11 komanso magulu atatu amene amagwilitsila nchito cinenelo camanja ca ku Honduras