Zamkati
April 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
YOPHUNZILA
JUNE 1-7, 2015
Akulu, Kodi Mumakonda Kuphunzitsa Ena?
TSAMBA 3 • NYIMBO: 123, 121
JUNE 8-14, 2015
Mmene Akulu Angathandizile Ena Kukhala Oyenelela Maudindo
TSAMBA 9 • NYIMBO: 45, 70
JUNE 15-21, 2015
Kodi Muli pa Ubwenzi Wolimba ndi Yehova?
TSAMBA 19 • NYIMBO: 91, 11
JUNE 22-28, 2015
Muzikhulupilila Yehova Nthawi Zonse
TSAMBA 24 • NYIMBO: 106, 49
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Akulu, Kodi Mumakonda Kuphunzitsa Ena?
▪ Mmene Akulu Angathandizile Ena Kukhala Oyenelela Maudindo
N’cifukwa ciani akulu afunika kuphunzitsa ena mumpingo? Nanga ndi zinthu ziti zimene akulu ayenela kucita kuti akwanitse kuphunzitsa ena? Kodi akulu ndiponso abale ena amene amaphunzitsidwa ndi akulu angaphunzile ciani kwa Samueli, Eliya, ndi Elisa? Nkhani ziŵilizi zikuyankha mafunso amenewa.
▪ Kodi Muli pa Ubwenzi Wolimba ndi Yehova?
▪ Muzikhulupilila Yehova Nthawi Zonse
Kukhala pa ubwenzi wabwino ndi Yehova kudzatithandiza kupilila mayeselo. Nkhani ziŵilizi zifotokoza mmene kukambilana ndi Yehova ndiponso kumudalila nthawi zonse kumalimbitsila ubwenzi wathu ndi iye.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
14 Madalitso “m’Nthawi Yabwino ndi m’Nthawi Yovuta”
29 Cifukwa Cake Kucotsa Munthu Mumpingo Ndi Makonzedwe Acikondi
PACIKUTO: Mkulu akuphunzitsa mtumiki wothandiza kucita ulaliki wapoyela wa m’mizinda ikuluikulu m’mbali mwa mseu wochedwa Haiphong Road, mumzinda wa Kowloon
HONG KONG
KULI ANTHU
7,234,800
OFALITSA
5,747
MAPHUNZILO A BAIBULO
6,382
ZOPOSA 180,000
Mashelufu a mawilo, matebulo, ndi zinthu zina zoikapo mabuku zinagulidwa kudzela mu ofesi ya nthambi ya ku Hong Kong ndi kutumizidwa padziko lonse