Zamkati
August 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI ZOPHUNZILA
SEPTEMBER 28, 2015–OCTOBER 4, 2015
Muzisinkhasinkha za Cikondi Cosatha ca Yehova
TSAMBA 9
OCTOBER 5-11, 2015
TSAMBA 14
OCTOBER 12-18, 2015
Konzekelani Kudzakhala m’Dziko Latsopano
TSAMBA 19
OCTOBER 19-25, 2015
Samalani ndi Anthu Ogwilizana Nao Masiku Ano Otsiliza
TSAMBA 24
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Muzisinkhasinkha za Cikondi Cosatha ca Yehova
Cikondi cimene Yehova amaonetsa anthu ake n’cosatha. Nkhaniyi ifotokoza mmene Yehova waonetsela cikondi cake. Kusinkhasinkha mmene Yehova wationetsela cikondi kudzatithandiza kulimbitsa ubwenzi wathu ndi iye.
▪ Yembekezelanibe!
▪ Konzekelani Kudzakhala m’Dziko Latsopano
Ngakhale kuti papita nthawi yaitali, tiyenela kukhalabe ndi ciyembekezo cakuti madalitso a Ufumu adzakwanilitsidwa. Tili ndi zifukwa zomveka zoyembekezela malonjezo a m’Baibulo. Nkhanizi zifotokoza mmene tingacitile zimenezi.
▪ Samalani ndi Anthu Ogwilizana Nao Masiku Ano Otsiliza
N’cifukwa ciani m’pofunika kusamala ndi anthu ogwilizana nao masiku ano otsiliza? Kodi Mau a Mulungu amatithandiza bwanji kucita zimenezi? Mafunso amenewa ndi ena adzayankhidwa m’nkhani ino.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
3 “Zilumba Zambili Zisangalale”
PACIKUTO: M’bale wacinyamata akucita ulaliki wamwai ndipo akuonetsa munthu wina vidiyo pa jw.org mu mzinda wa Esperanza
ARGENTINA
KULI ANTHU
42,670,000
OFALITSA
150,171
APAINIYA ANTHAWI ZONSE
18,538
MAPHUNZILO A BAIBULO
126,661
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2014)