Yophunzila
July 2016
NKHANI ZOPHUNZILA MLUNGU WA: AUGUST 29–SEPTEMBER 25, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CITHUNZI CA PACIKUTO:
DOMINICAN REPUBLIC
Mpainiya wapadela ali m’mbali mwa nyanja ku Las Terrenas, ndipo akuseŵenzetsa Baibulo kulalikila munthu amene wacoka kukolola ma kokonati
OFALITSA
37,536
MAPHUNZILO A BAIBULO
69,892
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2015)
120,103
Magazini iyi si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene imacitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ni zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zocilikizila nchitoyi, pitani pa www.jw.org.
Baibulo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lochedwa A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.