Yophunzila
AUGUST 2016
NKHANI ZOPHUNZILA M’MLUNGU WA: SEPTEMBER 26–OCTOBER 23, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CITHUNZI CA PACIKUTO:
HUNGARY
Kukamba zoona, kulalikila m’maŵa m’mbali mwa mtsinje wa Danube kumakondweletsa kwambili! Ofalitsa akulalikila mokondwela uthenga wa Ufumu kwa munthu wacidwi m’tawuni ya Vigadó mu Budapest ku Hungary
OFALITSA
22,582
APAINIYA
1,980
MAPHUNZILO A BAIBULO
12,163
Magazini iyi si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene imacitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ni zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zocilikizila nchitoyi, pitani pa www.jw.org.
Baibulo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lochedwa A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages