Zamkati
3 Napeza Cimwemwe Cifukwa Copatsa
MLUNGU WA SEPTEMBER 26–OCTOBER 2, 2016
8 Cikwati—Ciyambi na Cifuno Cake
MLUNGU WA OCTOBER 3-9, 2016
13 Kupangitsa Cikwati Cacikhiristu Kukhala Cacimwemwe
M’nkhani yoyamba tidzakambilana za ciyambi ca cikwati, mmene Cilamulo ca Mose cinatsogolela cikwati, ndi mfundo imene Yesu anakhazikitsa yokhuza cikwati. M’nkhani yaciŵili, tidzaona mmene Malemba amaunikila bwino udindo wa mwamuna ndi wa mkazi m’banja.
18 Fufuzani Cinthu Camtengo Wapatali Kuposa Golide
MLUNGU WA OCTOBER 10-16, 2016
20 Kodi Mumaona Kufunika Kopita Patsogolo Kuuzimu?
MLUNGU WA OCTOBER 17-23
25 Kodi Mumaona Kufunika Kophunzitsa Ena?
Ndife okondwela kuti nchito yolalikila za Ufumu yapita patsogolo kwambili. Koma kodi timaona kuti umenewu ni mwayi woonjezela utumiki wathu kwa Mulungu? Tingacite ciani kuti tipite patsogolo panthawi imodzi-modzi tithandizenso ophunzila Baibulo kupita patsogolo? N’cifukwa ciani pafunika kuti ena aphunzitsidwe? Nkhani ziŵilizi ziyankha mafunso ofunika amenewa.