Zamkati
MLUNGU WA OCTOBER 24-30, 2016
3 “Manja Anu Asakhale Olefuka”
MLUNGU WA OCTOBER 31, 2016–NOVEMBER 6, 2016
8 Cilimikani pa Kulimbana Kuti Mupeze Madalitso a Yehova
Mavuto na nkhawa za mu umoyo zingatipanikize ndi kucititsa manja athu ophiphilitsa kulefuka. Nkhani ziŵilizi zidzaonetsa mmene Yehova amatithandizila ndi dzanja lake lamphamvu kuti tipilile mavuto. Tidzaonanso mmene tingapitilizile kucilimika pa “kulimbana” kuti tipeze madalitso a Yehova.
13 Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi
14 Kuteteza Uthenga Wabwino Pamaso pa Akulu-akulu a Boma
MLUNGU WA NOVEMBER 7-13, 2016
17 Kodi Mavalidwe Anu Amalemekeza Mulungu?
Atumiki a Mulungu padziko lonse amafuna kuvala na kudzikonza moyenelela. Amavala zovala zooneka bwino, zoyela, ndi zololeka kudela la kwawo, komanso zogwilizana ndi mfundo za m’Malemba. Nanga mungacite ciani kuti mavalidwe anu azilemekeza Mulungu?
22 Ubwino Wotsatila Malangizo a Yehova
MLUNGU WA NOVEMBER 14-20, 2016
23 Wacicepele, Limbitsa Cikhulupililo Cako
MLUNGU WA NOVEMBER 21-27, 2016
28 Makolo, Thandizani Ana Anu Kukhala na Cikhulupililo
M’nkhani ziŵilizi, tidzaona mmene acicepele angaseŵenzetsele luso lawo la kulingalila kuti alimbitse cikhulupililo cawo na kuciteteza. Tidzaonanso mmene makolo acikhiristu angapezele njila zokondweletsa zothandizila ana awo kukulitsa cikhulupililo mwa Mulungu ndi Mau ake.