Yophunzila
SEPTEMBER 2016
NKHANI ZOPHUNZILA M’MLUNGU WA: OCTOBER 24–NOVEMBER 27, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CITHUNZI CA PACIKUTO:
FIJI
Abale na alongo amene akhala kumidzi yakutali ndi mzinda wa Suva, likulu la dziko la Fiji, amalalikila uthenga wabwino kwa aliyense
KULI ANTHU
887,027
OFALITSA
3,097
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2015)
11,845
Magazini iyi si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene imacitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ni zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zocilikizila nchitoyi, pitani pa www.jw.org.
Baibulo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lochedwa A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.