Yophunzila
OCTOBER 2016
NKHANI ZOPHUNZILA M’MLUNGU WA: NOVEMBER 28–DECEMBER 25, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CITHUNZI CA PACIKUTO:
KU LUXEMBOURG
Abale ali m’gawo la malonda, ndipo alalikila makanika pamalo okonzela mamotoka. Akuseŵenzetsa kapepa kauthenga kakuti Kodi Baibo Mumaiona Bwanji? kuti amukope cidwi pa Mau a Mulungu
KULI ANTHU
562,958
OFALITSA
2,058
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2015)
3,895
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene imacitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ni zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zocilikizila nchitoyi, pitani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lochedwa A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.