Yophunzila
NOVEMBER 2016
NKHANI ZOPHUNZILA M’MLUNGU WA: DECEMBER 26, 2016–JANUARY 29, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
KU ANGOLA
Mu mzinda wa Benguela, apainiya apadela atsogoza phunzilo la Baibo m’cinenelo ca manja, mwa kuseŵenzetsa kabulosha ka Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. Ofalitsa 10 osamva mu mzindawo anakondwela ngako kuti anthu 62 anapezeka pa Cikumbutso mu 2015
OFALITSA
115,948
MAPHUNZILO A BAIBO
502,848
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2015)
529,827
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ni zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.